Kelvinmbewe/mbert_Lusaka_Language_Analysis
Text Classification • 0.2B • Updated • 10
eng stringlengths 2 681 | nya stringlengths 1 797 |
|---|---|
' Here is your God , Israel , ' they cried ' who brought you out of the land of Egypt ! ' | ' Pano pali Mulungu wako , Israyeli , ' iwo anafuula ' yemwe anakutulutsa iwe kutuluka m 'dziko la Igupto ! ' |
The inexperienced ones will certainly take possession of foolishness , but the shrewd ones will bear knowledge as a headdress . | Achibwana amalandira cholowa cha utsiru ; koma ochenjera amavala nzeru ngati korona . |
Love never fails . | Chikondi sichitha nthaŵi zonse . |
Justice - Justice You Should Pursue | Chilungamo - Chilungamo Ndicho Mudzichitsata |
Remember Me , O My God , for Good | Inu Mulungu Wanga , Mundikumbukire pa Zabwino Zimene Ndinachita |
He Will Rise | Iye Adzauka |
TAKE a deep breath ! | KHAZIKITSANI mtima pansi ! |
Be Peaceable With All Men | Khalani mwa Mtendere ndi Anthu Onse |
To have children , to be happy and then to die . | Kukhala ndi ana , kukhala wachimwemwe ndiyeno kufa . |
The plenty belonging to the rich one is not permitting him to sleep . | Kukhuta kwa wolemera sikumgonetsa tulo . |
Make my joy full in that you are . . . doing nothing out of contentiousness or out of egotism , but with lowliness of mind considering that the others are superior to you , keeping an eye , not in personal interest upon just your own matters , but also in personal interest upon those of the others . | Kwaniritsani chimwemwe changa , . . musachite kanthu monga mwa chotetana , kapena monga mwa ulemerero wopanda pake , komatu ndi kudzichepetsa mtima , yense ayese anzake omposa iye mwini ; munthu yense asapenyerere zake za iye yekha , koma yense apenyererenso za mnzake . |
YOU HAVE ACTED FOOLISHLY | MWACHITA ZOPUSA |
Jehovah 's Witnesses Protected Me ! | Mboni za Yehova Zandichinjiriza ! |
God Is Greater Than Our Hearts | Mulungu Ali Wamkulu Woposa Mitima Yathu |
With oil you have greased my head . | Mwandidzoza mutu wanga mafuta . |
I FEEL scared and excited at the same time ! | NDIMAKHALA wamantha ndi wachimwemwe panthaŵi imodzimodzi ! |
I went flying off the tracks and fell down on the cinders just beyond . | Ndinanyamuka panjanjipo ndi kugwera m 'mapulusa a malasha amene anali m 'mbali mwake . |
' Tribulation in the Flesh ' | Nsautso M 'thupi |
The works of his hands are truth and judgment ; trustworthy are all the orders he gives , well supported forever , to time indefinite , done in truth and uprightness . | Ntchito za manja ake ndizo choonadi ndi chiweruzo ; malangizo ake onse ndiwo okhulupirika . Achirikizika ku nthawi za nthawi , achitika m 'choonadi ndi chilunjiko . |
We Are Missing Some Fundamental Element | Pali Mbali Ina Yofunika Imene Ikusoŵeka |
Why pay when you can get it free ? | Palibe chifukwa choperekera ndalama pa zinthu zomwe munthu ukhoza kuzipeza mwaulere . |
By the 1980s belief in the Devil had disappeared except among conservative Catholics , charismatics , conservative Protestants , Eastern Orthodox , Muslims - and a few occultists . | Pofika mu ma 1980 chikhulupiriro mwa Mdyerekezi chinazimiririka kuchotsapo kokha pakati pa Akatolika enieni , magulu opatuka kuchoka ku chiProtestanti , Aprotestanti enieni , Eastern Orthodox , Asilamu - ndi okhulupirira malaulo ochepa . |
I Have Not Sat With Men of Untruth | Sindinakhala Pansi ndi Anthu Achabe |
I 've Never Seen Anything Like This ! | Sindinaonepo Zonga Zimenezi ! |
We mustn 't let our spirit lose its sparkle | Tisalole kuti changu chathu chizirale n 'kusiya kunyezimira |
Jehovah , Please Let Me Serve You | Yehova , Ndiloleni Kuti Ndikutumikireni |
It is too much to bear . | Zimakhala zovuta zedi kuzipirira . |
" 2000 is , in a way , ' the largest expected event ' in human history ever , " suggests social researcher Bernward Joerges of Berlin , Germany . | " 2000 , m 'njira inayake , iri ' chochitika chachikulu choyembekezeredwa ' chikhalire m 'mbiri ya anthu , " akulingalira tero Bernward Joerges wofufuza zamayanjano a anthu wa ku Berlin , Jeremani . |
" When these delegates first arrived , they were very nervous and timid , " relates a Christian who helped with rooming . | " Alendo ameneŵa atangofika kumene , anali ndi nkhaŵa komanso manyazi kwambiri , " anatero Mkristu wina amene anali kuthandiza nawo pantchito yokonzera alendowo malo ogona . |
" My mother never sits down and has a talk with me , " complained one young girl . | " Amayi samakhala konse pansi kukambirana nane nkhani , " anadandaula msungwana wina wachichepere . |
" No , " she called back , a little bewildered . | " Ayi , " iye anatero , ali wododoma pang 'ono . |
" Faith is the assured expectation of things hoped for . " - HEBREWS 11 : 1 . | " Chikhulupiriro ndicho chikhazikitso cha zinthu zoyembekezeka , chiyesero cha zinthu zosapenyeka . " - AHEBRI 11 : 1 . |
Acts of " affection " can become increasingly inappropriate or unclean . | " Chikondi " chotere chingakule n 'kufika posafunikira kapenanso ponyansa . |
" The sad situation is that . . . the pharmaceutical industry isn 't looking for [ new treatments ] , " says Michael Ferguson , a molecular biologist at the University of Dundee , Scotland . | " Chomvetsa chisoni n 'chakuti . . . makampani opanga mankhwala sakufufuzanso mankhwala [ atsopano ] , " anatero Michael Ferguson yemwe ndi katswiri wa sayansi pa yunivesite ya Dundee ku Scotland . |
" Men in Western civilization have thus been thrown back wholly on themselves , and they find themselves wanting , " concludes The Columbia History of the World . | " Chotero , anthu m 'kutsungula Kwakumadzulo akhala akudalira kotheratu pa iwo okha , ndipo amadzipeza kukhala opereŵera , " ikumaliza motero The Columbia History of the World . |
" Granny " Hamilton became the first baptized publisher in County Longford . - 1 Thessalonians 2 : 13 . | " Gogo " Hamilton anakhala wofalitsa wobatizidwa woyamba mu County Longford . - 1 Atesalonika 2 : 13 . |
" He will swallow up death forever , and the Sovereign Lord Jehovah will wipe away the tears from all faces . " - Isaiah 25 : 8 . | " Iye adzameza imfa kwamuyaya ndipo Yehova , Ambuye Wamkulu Koposa , adzapukuta misozi pankhope zonse za anthu . " - Yesaya 25 : 8 . |
" Trust in Jehovah , you people , for all times , for in Jah Jehovah is the Rock of times indefinite . " - ISAIAH 26 : 4 . | " Khulupirirani Yehova anthu inu , nthaŵi zamuyaya , pakuti mwa Ya Yehova muli Thanthwe lachikhalire . " - YESAYA 26 : 4 , NW . |
[ God 's ] undeserved kindness that was toward me did not prove to be in vain , but I labored in excess of [ all the other apostles ] . " - 1 Corinthians 15 : 9 , 10 . | " Koma . . . chisomo [ cha Mulungu ] cha kwa ine sichinakhala chopanda pake , koma ndinagwirira ntchito yochuluka ya [ atumwi ena onse ] . " - 1 Akorinto 15 : 9 , 10 . |
" Be transformed by making your mind over , that you may prove to yourselves the good and acceptable and perfect will of God , " says the apostle Paul . | " Koma mukhale osandulika , mwa kukonzanso kwa mtima wanu , kuti mukazindikire chimene chili chifuno cha Mulungu , chabwino , ndi chokondweretsa , ndi changwiro , " akutero mtumwi Paulo . |
Liquid Gold ( olive oil ) , 4 / 08 | " Kukonda Kwambiri Anthu " ( Russia ) , 8 / 08 |
" Making new friends was really the key [ to adjusting ] , " says a youth named Brian whose family moved to the southern part of the United States . | " Kupanga mabwenzi atsopano kunalidi mfungulo [ ya kusintha ] , " akutero wachichepere wina wotchedwa Brian amene banja lake linasamukira kumbali yakummwera kwa United States . |
" The prevention of violence in the home and the reduction of family violence involve major structural changes for both the society and the family . " - Behind Closed Doors . | " Kupewa ndewu muukwati ndi kuchepetsa ndewu m 'banja kumaphatikizapo masinthidwe aakulu amachitidwe kwa onse aŵiri chitaganya ndi banja . " - Behind Closed Doors . |
" Career decision making is one of the major challenges young people face , " says the book Career Coaching Your Kids . | " Kusankha zinthu zoti mudzachite mutakula , n 'chinthu chovuta kwambiri kwa achinyamata , " linatero buku lakuti Career Coaching Your Kids . |
" In the fourth year of Jehoiakim the son of Josiah , the king of Judah , " the word of the Great Timekeeper " occurred to Jeremiah concerning all the people of Judah . " | " M 'chaka chachinayi cha ulamuliro wa Yehoyakimu mwana wa Yosiya , mfumu ya Yuda , " Yehova anauza Yeremiya mawu okhudza anthu a ku Yuda . |
" THE reasonable man " - English journalist Sir Alan Patrick Herbert dubbed him a mythical figure . | " MUNTHU wololera " - Mtolankhani Wachingelezi Bwana Alan Patrick Herbert anamutcha kukhala munthu wa m 'nthano chabe . |
" The calamitous days " of old age may hinder elderly Christians from serving Jehovah with the vigor they once had . - Ecclesiastes 12 : 1 . | " Masiku oipa " a ukalamba angalepheretse Akristu okalamba kutumikira Yehova ndi mphamvu monga kale . - Mlaliki 12 : 1 . |
This " reproductive seed " is God 's holy spirit . | " Mbewu " imeneyi ndiyo mzimu woyera wa Mulungu . |
" My Sister Never Gave Up on Me . " - YELENA VLADIMIROVNA SYOMINA | " Mchemwali wanga sanataye mtima . " - YELENA VLADIMIROVNA SYOMINA |
" A wife should not depart from her husband ; . . . and a husband should not leave his wife . " - 1 CORINTHIANS 7 : 10 , 11 . | " Mkazi asasiye mwamuna wake ; . . . mwamuna asalekane naye mkazi . " - 1 AKORINTO 7 : 10 , 11 . |
" Unlike many of my former friends who are now dead , I am alive and enjoying a happy family life , " says Adrian . | " Mosiyana ndi ambiri mwa azinzanga omwe tsopano anamwalira , ine ndili moyo ndipo ndili ndi banja lachimwemwe , " anatero Adrian . |
" This means everlasting life , " Jesus said in prayer , " their taking in knowledge of you , the only true God , and of the one whom you sent forth , Jesus Christ . " - John 17 : 3 . | " Moyo wosatha ndi uwu , " anatero Yesu m 'pemphero , " kuti akadziŵe Inu Mulungu woona yekha , ndi Yesu Kristu amene munam 'tuma . " - Yohane 17 : 3 . |
" Life , " he reminded me , " is far better traversed with as little baggage as possible . | " Moyotu , " iwo anandikumbutsa motero , " umakhala bwinopo ndi zinthu zochepa zakuthupi . |
" The birdcatcher , " Satan , sets many traps . | " Msodzi , " Satana , amatchera misampha yambirimbiri . |
" Choose for yourselves today whom you will serve , " he said . | " Mudzisankhire lero amene mudzamtumikira , " anatero . |
" That 's very impressive , Tiffany , that is very impressive , " said the teacher over and over again . | " N 'zochititsa chidwi kwambiri zimenezi , Tiffany , n 'zochititsa chidwi kwabasi , " anatero mphunzitsiyo mobwerezabwereza . |
" It is a privilege to receive an assignment from Jehovah God through his organization , " stated Mark Noumair , who served as a missionary in Kenya for 11 years and is now a Gilead instructor . | " Ndi mwaŵi kulandira gawo la ntchito kuchokera kwa Yehova Mulungu kudzera m 'gulu lake , " anatero Mark Noumair , amene anatumikira monga mmishonale ku Kenya kwa zaka 11 ndipo tsopano ndi mlangizi wa ku Gileadi . |
" They are the only ones to go from door to door with ' the good news , ' applying the Bible 's principles . " - Życie Literackie , Poland . | " Ndi okhawo omwe amapita khomo ndi khomo ndi ' uthenga wabwino , ' kugwiritsa ntchito mfundo zachikhalidwe chabwino za m 'Baibulo . " - Nyuzipepala ya Życie Literackie , ku Poland . |
" I jump for joy now , " he says , " when I think of what Jehovah God and Jesus Christ have done and will yet do for us ! " | " Ndimadumpha ndi chisangalalo tsopano , " iye akutero , " pamene ndiganiza za zimene Yehova Mulungu ndi Yesu Kristu atichitira ndipo adzatichitirabe ! " |
" My life is dedicated to the service of the Most High , " read the press report , " and I cannot serve two masters . " | " Ndinapatulira moyo wanga kuchita utumiki wa Wam 'mwambamwamba , " inasimba motero nyuzipepala , " ndipo sindingatumikire ambuye aŵiri . " |
" I prayed with my eyes open , " she recalls . | " Ndinapemphera osatseka maso , " iye anatero pokumbukira . |
" I learned responsibility , " says a young man named Eric . | " Ndinaphunzira kukhala wathayo , " akutero mnyamata wachichepere wotchedwa Eric . |
" I began this whole diet to control my weight , but now it 's controlling me , " says Jaimee . | " Ndinayamba khalidwe losala kudya limeneli chifukwa choti ndimafuna kuonda koma m 'malo mwake khalidweli likundilamulira , " akutero Jaimee . |
" You 're still a woman , and I 'm still a man . " ) | " Ndiwe mkazi ndithu , inenso ndine mwamuna ndithu . " ) |
" It is easy to let yourself go , to collapse and be consumed in self - pity " when exposed to a hostile or dangerous environment , says The SAS Survival Handbook . | " Nkwapafupi kugonja , kulephera ndi kungodzichitira chisoni " mutakhala pamalo oipa kapena angozi , ikutero The SAS Survival Handbook . |
At times I say things that everyone is probably thinking but that shouldn 't be said out loud . . . | " Nthawi zina ndimanena zinthu zomwe anthu enanso akuganiza koma zoti n 'zosayenera kunena pagulu . " - Allie |
You Can Remain Morally Clean , 11 / 1 | " Nthaŵi Yake Siinafike , " 9 / 15 |
" Sometimes we have pizza night , " says Sanchia , a girl from South Africa . | " Nthaŵi zina timadya pizza usiku , " akutero Sanchia , msungwana wa ku South Africa . |
" Studies show that the divorce rate in shift working families is 60 percent higher than for day workers in regular jobs , " says the book The 24 - Hour Society . | " Ofufuza amasonyeza kuti chiŵerengero cha kusudzulana m 'mabanja ogwira ntchito za mashifiti ndi chokwera ndi maperesenti 60 kuposa cha ogwira ntchito masana , " limatero buku lakuti The 24 - Hour Society . |
" With you [ God ] is the source of life . " - Psalm 36 : 9 . | " Pakuti inu [ Mulungu ] ndinu kasupe wa moyo . " - Salimo 36 : 9 . |
" When I 'm really in trouble or just do some stupid thing around the house , " laments 16 - year - old Karl , " they 'll say , ' Alan doesn 't do that ' or , ' Why can 't you clean up your room like Alan ? ' " | " Pamene ndiridi m 'vuto kapena ndachita kanthu kena kopusa panyumba , " anadandaula motero Karl wazaka 16 zakubadwa , " iwo adzati , ' Alan samachita zimenezo ' kapena kuti , ' Kodi ulekeranji kuyeretsa chipinda chako ngati Alan ? ' " |
" Although he was existing in God 's form , " Jesus " gave no consideration to a seizure , namely , that he should be equal to God . " | " Pokhala nawo maonekedwe a Mulungu , " Yesu " sanachiyesa cholanda kukhala wofanana ndi Mulungu . " |
" Concerning that day or the hour , " Jesus said , " nobody knows , neither the angels in heaven nor the Son , but the Father . " - Mark 13 : 32 , 33 . | " Ponena za tsikulo ndi ora , " Yesu anati , " palibe aliyense adziŵa , ngakhale angelo m 'mwamba kapena Mwana , koma Atate ndiwo . " - Marko 13 : 32 , 33 . |
" Find exquisite delight in Jehovah , and he will grant you the desires of your heart . " - PS . | " Sangalala mwa Yehova , ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako . " - SAL . |
" Ornament of All Galilee " ( Sepphoris ) , 6 / 1 | " Sankhani Moyo Kuti Mukhale ndi Moyo , " 6 / 1 |
" I shall not speak much with you anymore , " he says , " for the ruler of the world is coming . And he has no hold on me . " | " Sindidzalankhulanso zambiri ndi inu , " iye akutero , ' pakuti mkulu wa dziko lapansi adza ; ndipo alibe kanthu mwa Ine . ' |
" I no longer call you slaves , " he told them , " because a slave does not know what his master does . But I have called you friends , because all the things I have heard from my Father I have made known to you . " | " Sinditchanso inu akapolo , " anawauza tero , " chifukwa kapolo sadziŵa chimene mbuye wake achita ; koma ndatcha inu abwenzi ; chifukwa zonse zimene ndazimva kwa Atate wanga ndakudziŵitsani . " |
" We would not have been able to convince people in America , Canada or Japan to stop buying ivory if we were still selling it , " he replied . | " Sitikanatha kukhutiritsa maganizo mwamphamvu anthu a ku Amereka , Canada kapena Japan kuti aleke kugula minyanga ya njovu ngati tikanapitiriza kuigulitsa , " iye anayankha motero . |
" We are filled with gratefulness and appreciation for being Jehovah 's guests here in Berlin amid an international brotherhood . " - Bernd . | " Tadzazidwa ndi chikondwerereo ndi chiyamikiro cha kukhala alendo a Yehova muno mu Berlin pakati paubale wa m 'mitundu yonse . " - Bernd . |
" The church has been lying to us , " I said . | " Tchalitchi chakhala chikutinamiza , " ndinatero . |
" We have this treasure in earthen vessels , that the power beyond what is normal may be God 's and not that out of ourselves . " - 2 Corinthians 4 : 7 . | " Tili nacho chuma ichi m 'zotengera zadothi , kuti ukulu woposa wamphamvu ukhale wa Mulungu , wosachokera kwa ife . " - 2 AKORINTO 4 : 7 . |
" We became gentle in the midst of you , as when a nursing mother cherishes her own children . " - 1 THESSALONIANS 2 : 7 . | " Tinakhala ofatsa pakati pa inu , monga mmene mlezi afukatira ana ake a iye yekha . " - 1 ATESALONIKA 2 : 7 . |
" It should not be overlooked that one of [ Lucaris ' ] primary aims was to enlighten and uplift the educational level of his clergy and flock , which in the sixteenth and early seventeenth century had sunk to an extremely low point , " states one scholar . | " Tisaiwale mfundo yakuti chimodzi mwa zolinga zikuluzikulu za [ Lucaris ] chinali kuzindikiritsa ndi kukweza maphunziro a atsogoleri ake a chipembedzo ndi nkhosa , omwe m 'zaka za zana la 16 ndi kumayambiriro kwa zaka za zana la 17 anali ataloŵeratu pansi , " akutero katswiri wina wa zamaphunziro . |
" The day of Jehovah " was imminent , and his face was set against those ' withdrawing from him , ' that is , ' dedicating themselves away from following God . ' | " Tsiku la Yehova " linayandikira , ndipo nkhope yake inalunjikitsidwa motsutsana ndi awo ' ochoka kwa iye , ' kunena kuti , ' odzipereka iwo eni kuchoka ku kutsatira Mulungu . ' |
" Poverty in juxtaposition to great wealth " is one that was referred to by the Nigerian inspector - general of police . | " Umphaŵi woyendera limodzi ndi kulemera kwambiri " ndiwo chimodzi cha zinthuzo chimene mkulu wa apolisi wa ku Nigeria anatchula . |
" The vaccinator has replaced the postman as the most familiar visitor to home and hamlet , " notes a report on EPI . | " Wakatemera amachezera kwambiri nyumba ndi midzi kuposa wamtokoma , " lipoti lonena za EPI likutero . |
Those " meals " were delicious - and they nourished us well spiritually . | " Zakudya " zimenezo zinali zokoma ndipo zinatipatsa thanzi labwino lauzimu . |
" All things , therefore , that you want men to do to you , you also must likewise do to them . " - Matthew 7 : 12 . | " Zinthu zonse zimene mukufuna kuti anthu akuchitireni , inunso muwachitire zimenezo . " - Mateyo 7 : 12 . |
' He feared God and turned aside from bad . ' | ' Anaopa Mulungu ndi kupewa zoipa . ' |
' It is by your life course once you get there , ' he stressed . | ' Chiri mwa njira yanu ya moyo mwamsanga mutafika kumeneko , ' iye anagogomezera . |
' The Truth That Sets Us Free ' | ' Choonadi Chomwe Chimatimasula ' |
They That Go Down to the Sea in Ships | ' Iwo Akutsikira Kunyanja M 'zombo ' |
Be Content | ' Khalani Okhutira ' |
' Keeping my regulations , ' he said , " is wisdom on your part and understanding on your part before the eyes of the peoples who will hear of all these regulations , and they will certainly say , ' This great nation is undoubtedly a wise and understanding people . ' " - Deuteronomy 4 : 5 - 7 . | ' Kusunga maweruzo anga , ' iye anatero , " ndi nzeru zanu ndi chidziŵitso chanu pamaso pa mitundu ya anthu akumva malemba ndi kuti , Ndithu mtundu waukulu uwu , ndiwo anthu anzeru ndi akuzindikira . " - Deuteronomo 4 : 5 - 7 . |
' His Mouth Is a Source of Life ' | ' M 'kamwa Mwake Ndi Kasupe wa Moyo ' |
12 / 1 ' At River Coco , Turn Right , ' 9 / 1 | ' Mulungu Ndi Amene Amakulitsa ' ! |
I Will ' Climb Up Just as a Stag Does ' ( August 2006 ) Francesco Abbatemarco 's patience and humility really made me think . | ' Ndidzadumpha Ngati Nswala ' ( August 2006 ) Kupirira ndi kudzichepetsa kwa Francesco Abbatemarco , kunandichititsa kuganiza mozama . |
Do Not ' Follow the Crowd ' | ' Osatsata Unyinji wa Anthu ' |
It is God 's minister to you for your good . | ' Pakuti ndiye mtumiki wa Mulungu , kuchitira iwo zabwino . |
' Continue to Be Readjusted ' | ' Pitirizani Kukhala Wowongolereka ' |
This dataset contains parallel sentences in English and Chichewa (Malawi).
The dataset contains parallel sentences that can be used for:
If you use this dataset, please cite the citation guide of the original OPUS MT560 dataset.
This dataset is released under the Creative Commons Attribution 4.0 International License.